[male vocals] Mmmmmm
okondedwa
wanga
nimakukonda
namutima
wanga
ones,
Nika
kuona
nimathokoza
mulungu,
akupase
umoyo
wampamvu
ndi
thanzi
Doris
my
babe
babe
Oooo
zikomo
mulungu
wanga
Zikomo
mulungu
wanga
Ponipasa
okondedwa
Doris.
Doris
chonde
uwauze
azako
ones
Kuti
zachibwana
wasiya
lelo
pokhala
mukazi
wanga.
Koma
uzichepesi
kuti
mulungu
alamulile
banja
yatu.
Aku
chikazi
aku
chimuna
chonde
musaka
tipasule,
ndi
mau
onyoza,
nofuna
ulamulilo
munyumba
mwathu.
Chonde
mulungu
wanga
mukhale
khoswe
yathu
banjali.