Frobits
🎵 A song made on Frobits

Nyimbo Za Mulungu 347

Jacobs Gen · 🇿🇲 Zambia
0:000:00
Download Remix
Make your own song
Continues securely on the web
Lyrics

1 Tate,

ndili

mwana

wanu,

Nkana

ndinachimwa,

Ndingolirira

kwa

Inu;

Khululukireni.

Machimo

anga

ngambiri

Osawerengeka,

Ndingoyang'ana

kwa

Inu;

Khululukireni. 2

Ndinachimwa

poganiza

Ndi

polankhulanso,

M'ntchito

zanga

ndachimwanso;

Khululukireni.

Machimo

anga

ngambiri

Osawerengeka,

Ndingoyang'ana

kwa

Inu;

Khululukireni. 3

Ndinachita

mphulupulu,

Ndinakunyozani,

M'ntchito

zanga

ndalephera;

Khululukireni.

Machimo

anga

ngambiri

Machimo

anga

ngambiri

Osawerengeka,

Ndingoyang'ana

kwa

Inu;

Khululukireni. 4

Zonse

ndinakonda

kale

Ndi

zopanda

pake,

Sindikhuta

nazotu;

Khululukireni.

Machimo

anga

ngambiri

Machimo

anga

ngambiri

Osawerengeka,

Ndingoyang'ana

kwa

Inu;

Khululukireni.

Machimo

anga

ngambiri

Osawerengeka,

Ndingoyang'ana

kwa

Inu;

Khululukireni.

Done:

By

Mr

and

Mrs

Yotam

Mwale

More songs by Jacobs Listen to songs created by others
FROBITS